Luka 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yesu, pozindikira zimene anali kuganiza anawayankha kuti: “Kodi mukuganiza chiyani m’mitima mwanu?+ Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Yesu sanawakhulupirire+ kwenikweni chifukwa onsewo anali kuwadziwa.
22 Koma Yesu, pozindikira zimene anali kuganiza anawayankha kuti: “Kodi mukuganiza chiyani m’mitima mwanu?+