Maliko 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete.
4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete.