Maliko 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yakobo mwana wa Zebedayo, Yohane m’bale wa Yakobo+ (awiriwa anawatchanso a Boanege, kutanthauza Ana a Bingu), Machitidwe 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+
17 Yakobo mwana wa Zebedayo, Yohane m’bale wa Yakobo+ (awiriwa anawatchanso a Boanege, kutanthauza Ana a Bingu),
13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+