Maliko 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kunyanja. Chikhamu cha anthu ochokera ku Galileya ndi ku Yudeya chinam’tsatira.+
7 Koma Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kunyanja. Chikhamu cha anthu ochokera ku Galileya ndi ku Yudeya chinam’tsatira.+