Yesaya 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.+ Inde bwerani mudzagule vinyo+ ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo wake.+ Mateyu 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Odala ndi anthu amene akumva njala ndi ludzu+ la chilungamo, chifukwa adzakhuta.+
55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.+ Inde bwerani mudzagule vinyo+ ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo wake.+