Mateyu 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma kubadwa kwa Yesu Khristu kunali motere: Pa nthawi imene mayi ake Mariya anali atalonjezedwa+ ndi Yosefe kuti adzam’kwatira, Mariyayo anapezeka kuti ali ndi pakati mwa mzimu woyera+ asanatengane.
18 Koma kubadwa kwa Yesu Khristu kunali motere: Pa nthawi imene mayi ake Mariya anali atalonjezedwa+ ndi Yosefe kuti adzam’kwatira, Mariyayo anapezeka kuti ali ndi pakati mwa mzimu woyera+ asanatengane.