1 Mafumu 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anakumbatira mwanayo+ katatu ali pabedipo n’kufuulira Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wanga, chonde chititsani kuti moyo+ wa mwanayu ubwerere mwa iye.” Luka 8:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma iye anamugwira dzanja ndi kuitana kuti: “Mtsikana iwe, dzuka!”+ Yohane 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atanena zimenezi, anafuula mokweza mawu kuti: “Lazaro, tuluka!”+ Machitidwe 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+
21 Ndiyeno anakumbatira mwanayo+ katatu ali pabedipo n’kufuulira Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wanga, chonde chititsani kuti moyo+ wa mwanayu ubwerere mwa iye.”
40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+