Mateyu 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndithu ndikukuuzani anthu inu, Mwa onse obadwa kwa akazi,+ sanabadwepo wamkulu woposa Yohane M’batizi. Koma munthu amene ali wocheperapo mu ufumu+ wakumwamba ndi wamkulu kuposa iyeyu.
11 Ndithu ndikukuuzani anthu inu, Mwa onse obadwa kwa akazi,+ sanabadwepo wamkulu woposa Yohane M’batizi. Koma munthu amene ali wocheperapo mu ufumu+ wakumwamba ndi wamkulu kuposa iyeyu.