Genesis 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mumweko madzi pang’ono, ndiponso tikusambitseni mapazi.+ Kenako, mupumeko pansi pa mtengo.+ 1 Timoteyo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 wodziwika kuti anachita ntchito zabwino,+ analera bwino ana,+ anali kuchereza alendo,+ anasambitsa mapazi a oyera,+ anathandiza ena m’masautso,+ ndiponso anali kugwira mwakhama ntchito iliyonse yabwino.+
10 wodziwika kuti anachita ntchito zabwino,+ analera bwino ana,+ anali kuchereza alendo,+ anasambitsa mapazi a oyera,+ anathandiza ena m’masautso,+ ndiponso anali kugwira mwakhama ntchito iliyonse yabwino.+