Mateyu 27:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Komanso akazi ambiri ochokera ku Galileya amene ankatsatira Yesu kuti azimutumikira,+ anali komweko akuonerera chapatali ndithu.+ Maliko 15:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Panali amayi amene anali kuonerera chapatali ndithu,+ ena mwa iwo anali Mariya Mmagadala, Mariya mayi wa Yakobo Wamng’ono ndi Yose, komanso Salome,+
55 Komanso akazi ambiri ochokera ku Galileya amene ankatsatira Yesu kuti azimutumikira,+ anali komweko akuonerera chapatali ndithu.+
40 Panali amayi amene anali kuonerera chapatali ndithu,+ ena mwa iwo anali Mariya Mmagadala, Mariya mayi wa Yakobo Wamng’ono ndi Yose, komanso Salome,+