Luka 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amayiwa anali Mariya Mmagadala, Jowana+ ndi Mariya mayi wa Yakobo. Komanso amayi+ ena onse amene anali nawo pamodzi anali kuuza atumwi zinthu zimenezi.
10 Amayiwa anali Mariya Mmagadala, Jowana+ ndi Mariya mayi wa Yakobo. Komanso amayi+ ena onse amene anali nawo pamodzi anali kuuza atumwi zinthu zimenezi.