Mateyu 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso mbewu zina zinagwera paminga, ndipo mingazo zinakula ndi kulepheretsa mbewuzo kukula.+ Maliko 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mbewu zina zinagwera paminga, ndipo mingazo zinakula ndi kulepheretsa mbewuzo kukula, moti sizinabale chipatso chilichonse.+ Luka 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zimene zinagwera paminga, ndi anthu amene amva mawu a Mulungu. Koma chifukwa chotengeka ndi nkhawa, chuma ndi zosangalatsa za moyo uno,+ amalephera kukula bwino, ndipo zipatso zawo sizikhwima.+
7 Mbewu zina zinagwera paminga, ndipo mingazo zinakula ndi kulepheretsa mbewuzo kukula, moti sizinabale chipatso chilichonse.+
14 Zimene zinagwera paminga, ndi anthu amene amva mawu a Mulungu. Koma chifukwa chotengeka ndi nkhawa, chuma ndi zosangalatsa za moyo uno,+ amalephera kukula bwino, ndipo zipatso zawo sizikhwima.+