Mateyu 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma zofesedwa pamiyala, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuwavomereza mwamsanga ndiponso mwachimwemwe.+ Maliko 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Momwemonso, pali anthu amene amafesedwa pamiyala. Akangomva mawuwo, iwo amawalandira ndi chimwemwe.+
20 Koma zofesedwa pamiyala, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuwavomereza mwamsanga ndiponso mwachimwemwe.+
16 Momwemonso, pali anthu amene amafesedwa pamiyala. Akangomva mawuwo, iwo amawalandira ndi chimwemwe.+