Mateyu 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno pamene analowa m’ngalawa,+ ophunzira ake anam’tsatira. Maliko 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho atauza khamu la anthulo kuti lizipita, ophunzirawo anachoka naye pa ngalawa imene anakwera ija, koma analinso ndi ngalawa zina.+
36 Choncho atauza khamu la anthulo kuti lizipita, ophunzirawo anachoka naye pa ngalawa imene anakwera ija, koma analinso ndi ngalawa zina.+