Mateyu 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo iwo anapita kukam’dzutsa+ kuti: “Ambuye, tipulumutseni tikufa!” Maliko 4:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Yesu anali kumbuyo kwa ngalawayo akugona, atatsamira pilo. Chotero anam’dzutsa ndi kumufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi sizikukukhudzani kuti tikufa?”+
38 Koma Yesu anali kumbuyo kwa ngalawayo akugona, atatsamira pilo. Chotero anam’dzutsa ndi kumufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi sizikukukhudzani kuti tikufa?”+