Mateyu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+ Maliko 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndipo atafuula ndi mawu amphamvu,+ anati: “Kodi ndili nanu chiyani, Yesu, Mwana wa Mulungu Wam’mwambamwamba?+ Ndikukulumbiritsani+ pali Mulungu kuti musandizunze.”+ Luka 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Tili nanu chiyani,+ Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera wa Mulungu.”+
29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+
7 ndipo atafuula ndi mawu amphamvu,+ anati: “Kodi ndili nanu chiyani, Yesu, Mwana wa Mulungu Wam’mwambamwamba?+ Ndikukulumbiritsani+ pali Mulungu kuti musandizunze.”+
34 “Tili nanu chiyani,+ Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera wa Mulungu.”+