-
Maliko 9:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiyeno anafunsa bambo ake kuti: “Izi zakhala zikumuchitikira kwa nthawi yaitali bwanji?” Bamboyo anati: “Kuyambira ali mwana,
-