Levitiko 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake n’zogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ikhale yodetsedwa kwa inu. Deuteronomo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musamadyenso nkhumba+ chifukwa ndi ya ziboda zogawanika koma sibzikula. Imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu. Musamadye nyama yake ndipo ikafa musamaikhudze.+
7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake n’zogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ikhale yodetsedwa kwa inu.
8 Musamadyenso nkhumba+ chifukwa ndi ya ziboda zogawanika koma sibzikula. Imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu. Musamadye nyama yake ndipo ikafa musamaikhudze.+