-
Mateyu 8:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Koma amene anali kuyang’anira ziwetozo anathawa ndipo atalowa mumzinda anafotokoza zonse kuphatikizapo zimene zinachitikira amuna ogwidwa ndi ziwanda aja.
-