-
Maliko 5:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Komanso amene anaona zochitikazo, anawafotokozera mmene zinakhalira kwa munthu wogwidwa ziwanda uja ndiponso zimene zinachitikira nkhumba zija.
-