Maliko 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano pamene anali kukwera ngalawa, munthu amene anali ndi ziwanda uja anayamba kumuchonderera kuti aziyenda naye.+ Luka 18:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kumutsatira akulemekeza Mulungu.+ Komanso anthu onse, ataona zimenezi, anatamanda Mulungu.
18 Tsopano pamene anali kukwera ngalawa, munthu amene anali ndi ziwanda uja anayamba kumuchonderera kuti aziyenda naye.+
43 Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kumutsatira akulemekeza Mulungu.+ Komanso anthu onse, ataona zimenezi, anatamanda Mulungu.