Maliko 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komabe iye sanamulole, koma anamuuza kuti: “Pita kunyumba kwa achibale ako,+ ndipo ukawauze zonse zimene Yehova+ wakuchitira ndi chifundo+ chimene wakusonyeza.”
19 Komabe iye sanamulole, koma anamuuza kuti: “Pita kunyumba kwa achibale ako,+ ndipo ukawauze zonse zimene Yehova+ wakuchitira ndi chifundo+ chimene wakusonyeza.”