Maliko 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yesu atawolokanso pangalawa kubwerera kutsidya lina, khamu lalikulu la anthu linasonkhana kwa iye, ndipo iye anali m’mphepete mwa nyanja.+
21 Yesu atawolokanso pangalawa kubwerera kutsidya lina, khamu lalikulu la anthu linasonkhana kwa iye, ndipo iye anali m’mphepete mwa nyanja.+