Maliko 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo ananyamuka naye limodzi, ndipo khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira ndi kumam’panikiza.+
24 Pamenepo ananyamuka naye limodzi, ndipo khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira ndi kumam’panikiza.+