Luka 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsiku lina iye anali kuphunzitsa, ndipo Afarisi ndi aphunzitsi a chilamulo ochokera m’midzi yonse ya Galileya, ku Yudeya ndi ku Yerusalemu anakhala pansi pamalo omwewo. Ndipo mphamvu ya Yehova inali pa iye kuti athe kuchiritsa.+
17 Tsiku lina iye anali kuphunzitsa, ndipo Afarisi ndi aphunzitsi a chilamulo ochokera m’midzi yonse ya Galileya, ku Yudeya ndi ku Yerusalemu anakhala pansi pamalo omwewo. Ndipo mphamvu ya Yehova inali pa iye kuti athe kuchiritsa.+