Maliko 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma mayiyo, anachita mantha ndi kuyamba kunjenjemera, podziwa zimene zam’chitikira. Ndipo anafika pafupi n’kugwada pamaso pake ndi kumuuza zoona zonse.+
33 Koma mayiyo, anachita mantha ndi kuyamba kunjenjemera, podziwa zimene zam’chitikira. Ndipo anafika pafupi n’kugwada pamaso pake ndi kumuuza zoona zonse.+