Maliko 5:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ali mkati molankhula, panafika amuna ena ochokera kunyumba kwa mtsogoleri wa sunagoge uja ndipo anamuuza kuti: “Mwana wanu uja wamwalira! Musiyeni mphunzitsiyu musamuvutitse.”+
35 Ali mkati molankhula, panafika amuna ena ochokera kunyumba kwa mtsogoleri wa sunagoge uja ndipo anamuuza kuti: “Mwana wanu uja wamwalira! Musiyeni mphunzitsiyu musamuvutitse.”+