36 Koma Davide+ anakwaniritsa chifuniro cha Mulungu mu nthawi ya m’badwo wake, ndipo anagona mu imfa ndi kuikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake, moti thupi lake linavunda.+
39 Mkazi ndi womangika pa nthawi yonse imene mwamuna wake ali moyo.+ Komano mwamuna wake akamwalira, mkaziyo ndi womasuka kukwatiwa ndi aliyense amene akufuna, koma akwatiwe mwa Ambuye.+