Mateyu 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, pakuti mtsikanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola.+ Maliko 5:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola. Koma atawatulutsa onsewo, anatenga bambo ndi mayi a mwanayo ndi amene anali naye aja, ndipo analowa kumene kunali mwanayo.+
24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, pakuti mtsikanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola.+
40 Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola. Koma atawatulutsa onsewo, anatenga bambo ndi mayi a mwanayo ndi amene anali naye aja, ndipo analowa kumene kunali mwanayo.+