Mateyu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu atamaliza kupereka malangizo kwa ophunzira ake 12 aja, anachoka kumeneko n’kupita kukaphunzitsa ndi kukalalikira kumizinda ina.+ Maliko 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho anapita ndi kukalalikira kuti anthu alape.+
11 Tsopano Yesu atamaliza kupereka malangizo kwa ophunzira ake 12 aja, anachoka kumeneko n’kupita kukaphunzitsa ndi kukalalikira kumizinda ina.+