Mateyu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo anauza atumiki ake kuti: “Ameneyu ndi Yohane M’batizi. Anauka kwa akufa, ndipo n’chifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+ Maliko 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano izi zinamveka kwa Mfumu Herode,* chifukwa dzina la Yesu linamveka paliponse. Anthu anali kunena kuti: “Yohane m’batizi wauka kwa akufa, ndipo pa chifukwa chimenechi akuchita ntchito zamphamvu.”+ Maliko 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anamuyankha kuti: “Akumanena kuti Yohane M’batizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumati Mmodzi wa aneneri.”+ Luka 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Poyankha iwo anati: “Amati ndinu Yohane M’batizi. Koma ena amati ndinu Eliya. Enanso amati mmodzi wa aneneri akale wauka.”+
2 ndipo anauza atumiki ake kuti: “Ameneyu ndi Yohane M’batizi. Anauka kwa akufa, ndipo n’chifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+
14 Tsopano izi zinamveka kwa Mfumu Herode,* chifukwa dzina la Yesu linamveka paliponse. Anthu anali kunena kuti: “Yohane m’batizi wauka kwa akufa, ndipo pa chifukwa chimenechi akuchita ntchito zamphamvu.”+
28 Iwo anamuyankha kuti: “Akumanena kuti Yohane M’batizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumati Mmodzi wa aneneri.”+
19 Poyankha iwo anati: “Amati ndinu Yohane M’batizi. Koma ena amati ndinu Eliya. Enanso amati mmodzi wa aneneri akale wauka.”+