Mateyu 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano atafika m’zigawo za Kaisareya wa Filipi, Yesu anafunsa ophunzira ake kuti: “Kodi anthu akumanena kuti Mwana wa munthu ndani?”+ Maliko 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kumidzi ya Kaisareya wa Filipi. Ali m’njira, anayamba kufunsa ophunzira ake, kuti: “Kodi anthu akumanena kuti ine ndine ndani?”+
13 Tsopano atafika m’zigawo za Kaisareya wa Filipi, Yesu anafunsa ophunzira ake kuti: “Kodi anthu akumanena kuti Mwana wa munthu ndani?”+
27 Tsopano Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kumidzi ya Kaisareya wa Filipi. Ali m’njira, anayamba kufunsa ophunzira ake, kuti: “Kodi anthu akumanena kuti ine ndine ndani?”+