Genesis 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Sarai anali wosabereka,+ choncho analibe mwana. Salimo 113:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akuchititsa mkazi wosabereka kukhala m’nyumba+Monga mayi wosangalala wa ana aamuna.+Tamandani Ya, anthu inu!+
9 Akuchititsa mkazi wosabereka kukhala m’nyumba+Monga mayi wosangalala wa ana aamuna.+Tamandani Ya, anthu inu!+