Mateyu 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atakweza maso awo, anaona kuti palibe wina aliyense koma Yesu yekha.+ Maliko 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo iwo anayang’ana uku ndi uku, ndipo anangoona kuti palibe wina aliyense, koma Yesu yekha basi.+
8 Pamenepo iwo anayang’ana uku ndi uku, ndipo anangoona kuti palibe wina aliyense, koma Yesu yekha basi.+