Maliko 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo iwo anapita naye kwa Yesu. Koma mzimuwo utamuona, nthawi yomweyo unatsalimitsa mwanayo. Atagwa pansi anagubudukagubuduka ndi kuchita thovu.+ Luka 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo wakufayo anadzuka ndi kukhala tsonga, ndipo anayamba kulankhula. Kenako anam’pereka kwa mayi ake.+
20 Pamenepo iwo anapita naye kwa Yesu. Koma mzimuwo utamuona, nthawi yomweyo unatsalimitsa mwanayo. Atagwa pansi anagubudukagubuduka ndi kuchita thovu.+
15 Pamenepo wakufayo anadzuka ndi kukhala tsonga, ndipo anayamba kulankhula. Kenako anam’pereka kwa mayi ake.+