Miyambo 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu asanagwe, mtima wake umadzikweza,+ ndipo asanapeze ulemerero, amadzichepetsa.+ Mateyu 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero, aliyense amene adzadzichepetsa+ ngati mwana wamng’ono uyu ndi amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba.+ Mateyu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense wodzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense wodzichepetsa adzakwezedwa.+
4 Chotero, aliyense amene adzadzichepetsa+ ngati mwana wamng’ono uyu ndi amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba.+