Maliko 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife taona munthu wina akutulutsa ziwanda m’dzina lanu, choncho tinamuletsa,+ chifukwa sanali kuyenda ndi ife.”+
38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife taona munthu wina akutulutsa ziwanda m’dzina lanu, choncho tinamuletsa,+ chifukwa sanali kuyenda ndi ife.”+