Aefeso 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho samalani kwambiri kuti mmene mukuyendera+ si monga anthu opanda nzeru, koma ngati anzeru.