Luka 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene iwo anachita.+ Atatero anawatenga ndi kupita nawo kwaokhaokha+ mumzinda wotchedwa Betsaida.
10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene iwo anachita.+ Atatero anawatenga ndi kupita nawo kwaokhaokha+ mumzinda wotchedwa Betsaida.