Mateyu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yesu atabadwa ku Betelehemu+ wa Yudeya m’masiku a mfumu Herode,*+ okhulupirira nyenyezi+ ochokera kumadera a kum’mawa anabwera ku Yerusalemu.
2 Yesu atabadwa ku Betelehemu+ wa Yudeya m’masiku a mfumu Herode,*+ okhulupirira nyenyezi+ ochokera kumadera a kum’mawa anabwera ku Yerusalemu.