Mateyu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba. 1 Timoteyo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uwalamule kuti azichita zabwino,+ akhale olemera pa ntchito zabwino,+ owolowa manja, okonzeka kugawira ena,+ Yakobo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi?
20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba.
18 Uwalamule kuti azichita zabwino,+ akhale olemera pa ntchito zabwino,+ owolowa manja, okonzeka kugawira ena,+
5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi?