Yobu 38:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya? Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapatsa zilombo chakudya chawo,+Amapatsanso ana a makwangwala chakudya chimene amalirira.+
41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?