Mateyu 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Komanso pa nkhani ya zovala, n’chifukwa chiyani mukuda nkhawa? Phunzirani pa mmene maluwa+ akutchire amakulira. Sagwira ntchito, ndiponso sawomba nsalu.
28 Komanso pa nkhani ya zovala, n’chifukwa chiyani mukuda nkhawa? Phunzirani pa mmene maluwa+ akutchire amakulira. Sagwira ntchito, ndiponso sawomba nsalu.