Mateyu 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano ngati Mulungu amaveka chotero zomera zakutchire, zimene zimangokhalapo lero lokha, mawa n’kuzisonkheza pamoto, kodi iye sadzakuvekani kuposa pamenepo, achikhulupiriro chochepa inu?+
30 Tsopano ngati Mulungu amaveka chotero zomera zakutchire, zimene zimangokhalapo lero lokha, mawa n’kuzisonkheza pamoto, kodi iye sadzakuvekani kuposa pamenepo, achikhulupiriro chochepa inu?+