Mateyu 24:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kapolo ameneyu adzakhala wodala+ ngati mbuye wake pobwera adzam’peza akuchita zimenezo! Mateyu 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atanyamuka kupita kukagula, mkwati anafika, ndipo anamwali okonzekerawo analowa naye limodzi m’nyumba imene munali phwando laukwati,+ ndipo chitseko chinatsekedwa.
10 Atanyamuka kupita kukagula, mkwati anafika, ndipo anamwali okonzekerawo analowa naye limodzi m’nyumba imene munali phwando laukwati,+ ndipo chitseko chinatsekedwa.