Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 “Koma dziwani ichi: Ngati mwininyumba angadziwe nthawi yobwera mbala,+ angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.

  • 1 Atesalonika 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti inu eni mukudziwa bwino kuti tsiku la Yehova*+ lidzabwera ndendende ngati mbala usiku.+

  • 2 Petulo 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komabe, tsiku la Yehova+ lidzafika ngati mbala,+ pamene kumwamba kudzachoka+ ndi mkokomo waukulu,+ koma zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri n’kusungunuka,+ ndipo dziko lapansi+ ndi ntchito zake zidzaonekera poyera.+

  • Chivumbulutso 16:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Taona! Ndikubwera ngati mbala.+ Wodala ndi amene akhalabe maso+ ndi kukhalabe chivalire malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu n’kuona maliseche ake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena