Genesis 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Abulahamu anauza mtumiki wake yemwe anali wamkulu koposa m’nyumba yake, ndi woyang’anira zinthu zake zonse,+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga.+ 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+ 2 Atesalonika 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho abale, khalani olimba+ ndipo gwirani mwamphamvu miyambo+ imene munaphunzitsidwa, kaya mwa uthenga wapakamwa kapena mwa kalata yochokera kwa ife. 1 Petulo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Molingana ndi mphatso imene aliyense walandira, igwiritseni ntchito potumikirana monga oyang’anira abwino amene alandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene wakusonyeza m’njira zosiyanasiyana.+
2 Chotero Abulahamu anauza mtumiki wake yemwe anali wamkulu koposa m’nyumba yake, ndi woyang’anira zinthu zake zonse,+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga.+
15 Choncho abale, khalani olimba+ ndipo gwirani mwamphamvu miyambo+ imene munaphunzitsidwa, kaya mwa uthenga wapakamwa kapena mwa kalata yochokera kwa ife.
10 Molingana ndi mphatso imene aliyense walandira, igwiritseni ntchito potumikirana monga oyang’anira abwino amene alandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene wakusonyeza m’njira zosiyanasiyana.+