Mateyu 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Musaganize kuti ndinabweretsa mtendere padziko lapansi, sindinabweretse mtendere+ koma lupanga.