Machitidwe 5:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako kunali Yudasi Mgalileya m’masiku a kalembera.+ Iyeyu anakopa anthu ndipo anamutsatira. Koma munthu ameneyunso anafa, ndipo onse amene anali kumutsatira anabalalikabalalika.
37 Kenako kunali Yudasi Mgalileya m’masiku a kalembera.+ Iyeyu anakopa anthu ndipo anamutsatira. Koma munthu ameneyunso anafa, ndipo onse amene anali kumutsatira anabalalikabalalika.