Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wako.+ Usagwire ntchito iliyonse,+ iweyo kapena mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi, ng’ombe yako yamphongo, bulu wako, chiweto chako chilichonse, kapena mlendo wokhala mumzinda wanu,+ kuti nayenso kapolo wako wamwamuna ndi kapolo wako wamkazi, azipumula monga iwe.+

  • Mateyu 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mmenemo munali munthu wopuwala dzanja.+ Chotero iwo anam’funsa kuti, “Kodi n’kololeka kuchiritsa odwala tsiku la sabata?” Cholinga chawo chinali kum’peza chifukwa, kuti amuzenge mlandu.+

  • Maliko 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho Afarisi anali kumuyang’anitsitsa kuti aone ngati angachiritse munthuyo pa sabata, n’cholinga chakuti amuimbe mlandu.+

  • Yohane 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Atamva zimenezi Ayudawo anayamba kuvutitsa+ Yesu, chifukwa anali kuchita zinthu zimenezi pa Sabata.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena